
GOSH!Mighty Wanderers yatchona ku Mozambique, Bus yaonongeka
Timu ya Mighty Wanderers yalephera kufika mdziko muno dzulo kuchokera ku Mozambique komwe imatenga nawo gawo mu Mpikisano wa Songo International Tournament kumapeto a sabata yatha. Manoma amayenera kufika kuno ku mudzi dzulo koma kamba ka kuonongeka kwa …